Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Call Website Contact the business

Fighting Against Hiv/Aids and Sti PHUNZILANI ZA HIV/AIDS NDIMATENDA OPATSILANA POGONANA MULI KUNYUMBA. UTHENGA WA CHIPATALA.PANGANI FOLLOW PAGE LATHU.
*ART AND STI CLINICAL MENTOR*
(1)

13/11/2026

moyowu ulingati flames yopanda utsi

13/11/2026

Kupita kwamabungwe othsndiza ku HIV chutanthauza chani?.
Anthuwa akufuna kuti tiziimile patokha. koma ma ARV azipezeka, ma service onse azipedzeka koma zonse ziziyendesedwa ndi ogwira tchito muboma . ndipo thandizo lonse muzikalipeza.

Apatu timvane bwino bwino.mabungwe ambiri amene amathandiza program ya HIV akusanzika.ndipofunika kuti tiyikepo tokha mt...
13/11/2026

Apatu timvane bwino bwino.
mabungwe ambiri amene amathandiza program ya HIV akusanzika.
ndipofunika kuti tiyikepo tokha mtima pankhani yokhuza HIV . kuyezetsa, kukatenga ma ARV komaso kumwa ma ARV mwandondomeko.
pali ena timayambilaso kumwa akatilondola kunyumba. mwina zinthu ngati izi sizionekaso. ndikofunika kuikapo nokha mtima

Take charge of yourself by starting with HIV testing .
13/11/2026

Take charge of yourself by starting with HIV testing .

mpaka lero ena sakuziwabe kuti HIV si AIDs.
13/11/2026

mpaka lero ena sakuziwabe kuti HIV si AIDs.

13/11/2026

Hallo admn
ine ndikumva zizindikilo zonse xa HIV koma ndikapita ku chipatala akuti ndilibe. ine ndasiya kukhulupilila zoyezela zija.

Nthawi zina mumene timaganizila ,zimabalalisa wezi.imagine akuti uli negative basi sukugwirizana mazo

13/11/2026

Good morning team .
ndizotheka ukuwelengawe uli ndi kachilombo ka HIV kungoti sunayezese chabe.
lero Friday tiyeni tikayezese

Goodnight team always use condom
12/11/2026

Goodnight team
always use condom

mkuchedwa pati???syphilis(chindoko chamumagazi) nthawi zambiri simaziwika kuti ili muthupi koma zotsatila zake ndizoonon...
12/11/2026

mkuchedwa pati???
syphilis(chindoko chamumagazi) nthawi zambiri simaziwika kuti ili muthupi koma zotsatila zake ndizoononga komaso kupha. imakwanisa kukhala muthupi lamunthu kuposa zaka 20 ngati simunalandile thandizo.
pakakhala mwayi tiyeni tiziyexesako aka.
pano nde kali paliponse

12/11/2026

kwa zaka 10 akhala akubwera kuzalandila ma ARV.
lero angofikila ndiyaku ndufuna mndiyeze magazi mulungu wanga ndiwatheka bwanji.

kuwafunsa kuti nkhaniyitu mwayambira panjila.
akuti ndati ndiyezeni magadzi ndukhulupilila kuti ndachilisidwa ndi mwazi wa yesu ngati simkufuna ndikayezesa kwina.

koma amalawi inuyo, osanamizana kumeneko . pemphelani uku mzimwa ma ARV anu

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fighting Against Hiv/Aids and Sti posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Fighting Against Hiv/Aids and Sti:

Shortcuts

Share