18/10/2026
CHIDZIWITSO CHA NURSE REACH SERVICES!
Ndife okondwa kukudziwitsani za NurseReach Services, Chipatala chatsopano chopereka chithandizo cha zaumoyo kudzera pa ukadaulo wamakono, yomwe yakhazikitsidwa ndi NyasaHelp 3H Network Health Care Services.
M***a kulumikizana ndi akatswiri a zaumoyo popanda kupita ku chipatala.
π NTCHITO ZATHU ZIKUPHATIKIZAPO:
π©Ί Kukaonana ndi anamwino kuti mupeze uphungu ndi chithandizo cha zaumoyo.
π¨ββοΈ Kukaonana ndi azachipatala kudzera pa foni kapena ukadaulo wina.
π Uphungu wa zaumoyo kuti muphunzire mmene mungasamalire thanzi lanu.
π Chisamaliro chapadera cha kunyumba komanso chithandizo chotsatira kwa odwala amene akufunika kuyang'aniridwa.
π₯ Kuthandiza odwala kupeza chithandizo china powalumikiza ndi zipatala kapena akatswiri oyenera malinga ndi zosowa zawo.
π MALO AMENE MUNGATIPEZE
Bumbunyika ndi Section 9, Jenda.
π± WhatsApp: 0886409761
πΆπ½ββοΈ TAYAMBA NDI NTCHITO YATHU YA SOFT LAUNCH!
Tikuyamba ndikafufuku wa matenda kudzindikira omwe akufunika chithandizo cha zaumoyo msanga makamaka nthenda zagonagona(Active Case Finding).
Ntchitoyi ikuphatikizapo kuyendera anthu kunyumba ndi nyumba, kuwunika thanzi lawo komanso kuwathandiza kudziwa nthawi yoyenera kufunafuna chithandizo cha akatswiri a zaumoyo.
Musadikire mpaka matenda atakula! Lumikizanani nafe kuti mudziwe zambiri zokhudza ntchito zomwe zilipo, nthawi zokumana ndi akatswiri a zaumoyo komanso ndalama zolipirira chithandizo.
π NurseReach Services β Chithandizo cha Zaumoyo, Kulikonse Kumene Muli!
Professional Care β Right Where You Are.
Visit and book appointment on our online clinic Portal :
Free HTML Templates